Mateyu 1:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo pambuyo pake pa kutengedwako ku Babiloni, Yekoniya anabala Sealatiele; ndi Sealatiele anabala Zerubabele; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo pambuyo pake pa kutengedwako ku Babiloni, Yekoniya anabala Sealatiele; ndi Sealatiele anabala Zerubabele; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Aisraele atatengedwa ukapolo kupita ku Babiloni, Yekoniya adabereka Salatiele, Salatiele adabereka Zerubabele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ali ku ukapolo ku Babuloni, Yekoniya anabereka Salatieli, Salatieli anabereka Zerubabeli. Onani mutuwo |
Ndipo kunali chaka cha makumi atatu mphambu zisanu ndi ziwiri cha kumtenga ndende Yehoyakini mfumu ya Yuda, mwezi wakhumi ndi ziwiri, tsiku la makumi awiri mphambu asanu ndi awiri la mwezi, Evili-Merodaki mfumu ya Babiloni anamuweramutsa mutu wake wa Yehoyakini mfumu ya Yuda atuluke m'kaidi, chaka cholowa iye ufumu wake;