Mateyu 1:13 - Buku Lopatulika13 ndi Zerubabele anabala Abihudi; ndi Abihudi anabala Eliyakimu; ndi Eliyakimu anabala Azoro; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 ndi Zerubabele anabala Abihudi; ndi Abihudi anabala Eliyakimu; ndi Eliyakimu anabala Azoro; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Zerubabele adabereka Abihudi, Abihudi adabereka Eliyakimu, Eliyakimu adabereka Azoro. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Zerubabeli anabereka Abiudi, Abiudi anabereka Eliakimu, Eliakimu anabereka Azoro. Onani mutuwo |