Mateyu 1:1 - Buku Lopatulika1 Buku la kubadwa kwa Yesu Khristu, mwana wa Davide, mwana wa Abrahamu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Buku la kubadwa kwa Yesu Khristu, mwana wa Davide, mwana wa Abrahamu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Yesu Khristu, makolo ake anali Davide ndi Abrahamu. Motsatanatsatana maina a makolo ake onse ndi aŵa: Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Buku lofotokoza za mʼbado wa Yesu Khristu mwana wa Davide, mwana wa Abrahamu: Onani mutuwo |