Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 96:5 - Buku Lopatulika

5 Pakuti milungu yonse ya mitundu ya anthu ndiyo mafano, koma Yehova analenga zakumwamba.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Pakuti milungu yonse ya mitundu ya anthu ndiyo mafano, koma Yehova analenga zakumwamba.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Paja milungu yonse ya mitundu ina ya anthu ndi mafano chabe. Koma Chauta ndiye adalenga zakumwamba.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Pakuti milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi mafano, koma Yehova analenga mayiko akumwamba.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 96:5
15 Mawu Ofanana  

Pachiyambi Mulungu adalenga kumwamba ndi dziko lapansi.


Odalitsika inu a kwa Yehova, wakulenga kumwamba ndi dziko lapansi.


Mafano a amitundu ndiwo siliva ndi golide, ntchito ya manja a anthu.


Akuwapanga adzafanana nao; inde, onse akuwakhulupirira.


munthu ndani kuti mumkumbukira? Ndi mwana wa munthu kuti mucheza naye?


Taona, iwo onse, ntchito zao zikhala zopanda pake ndi zachabe; mafano ao osungunula ndiwo mphepo ndi masokonezo.


Atero Mulungu Yehova, Iye amene analenga thambo, nalifutukula, nayala ponse dziko lapansi, ndi chimene chituluka m'menemo, Iye amene amapatsa anthu a m'menemo mpweya, ndi mzimu kwa iwo amene ayenda m'menemo;


Ndipo muona ndi kumva, kuti si pa Efeso pokha, koma monga pa Asiya ponse, Paulo uyu akopa ndi kutembenutsa anthu ambiri, ndi kuti, Si milungu iyi imene ipangidwa ndi manja:


Tsono kunena za kudya zoperekedwa nsembe kwa mafano, tidziwa kuti fano silili kanthu padziko lapansi, ndi kuti palibe Mulungu koma mmodzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa