Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 96:1 - Buku Lopatulika

1 Muimbireni Yehova nyimbo yatsopano; muimbireni Yehova, inu, dziko lonse lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Muimbireni Yehova nyimbo yatsopano; muimbireni Yehova, inu, dziko lonse lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Imbirani Chauta nyimbo yatsopano! Imbirani Chauta, anthu a m'dziko lonse lapansi!

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano; Imbirani Yehova dziko lonse lapansi.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 96:1
10 Mawu Ofanana  

Aleluya, Muimbireni Yehova nyimbo yatsopano, ndi chilemekezo chake mu msonkhano wa okondedwa ake.


Mumuimbire Iye nyimbo yatsopano; muimbe mwaluso kumveketsa mau.


Dziko lonse lapansi lidzakugwadirani, ndipo lidzakuimbirani; ndzaimbira dzina lanu.


Imbirani Mulungu, maufumu a dziko lapansi inu; imbirani Ambuye zomlemekeza.


Muimbireni Yehova nyimbo yatsopano; popeza anachita zodabwitsa: Dzanja lake lamanja, mkono wake woyera, zinamchitira chipulumutso.


Ndiponso, Tamandani Ambuye, inu a mitundu yonse; ndipo anthu onse amtamande.


ndipo aimba ngati nyimbo yatsopano kumpando wachifumu, ndi pamaso pa zamoyo zinai, ndi akulu; ndipo palibe munthu anakhoza kuphunzira nyimboyi, koma zikwi zana mphambu makumi anai kudza anai, ogulidwa kuchokera kudziko.


Ndipo aimba nyimbo yatsopano, ndi kunena, Muyenera kulandira bukulo, ndi kumasula zizindikiro zake; chifukwa mwaphedwa, ndipo mwagulira Mulungu ndi mwazi wanu anthu a mafuko onse, ndi manenedwe onse, ndi mitundu yonse,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa