Masalimo 94:9 - Buku Lopatulika9 Kodi Iye wakupanga khutu ngwosamva? Kodi Iye wakuumba diso ngwosapenya? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Kodi Iye wakupanga khutu ngwosamva? Kodi Iye wakuumba diso ngwosapenya? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Kodi amene adalenga makutu, sangathe kumva? Kodi amene adapanga maso, sangathe kupenya? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Kodi Iye amene anapanga khutu sangathe kumva? Kodi Iye amene anapanga diso sangathe kuona? Onani mutuwo |