Masalimo 94:8 - Buku Lopatulika8 Zindikirani, opulukira inu mwa anthu; ndipo opusa inu, mudzachita mwanzeru liti? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Zindikirani, opulukira inu mwa anthu; ndipo opusa inu, mudzachita mwanzeru liti? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Mvetsani anthu opusa kwambirinu. Zitsiru inu, mudzakhala ndi nzeru liti? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Samalani, inu anthu opanda nzeru pakati pa anthu; zitsiru inu, kodi mudzakhala liti anzeru? Onani mutuwo |