Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 94:7 - Buku Lopatulika

7 Ndipo amati, Yehova sachipenya, ndi Mulungu wa Yakobo sachisamalira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndipo amati, Yehova sachipenya, ndi Mulungu wa Yakobo sachisamalira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Kenaka amati, “Chauta sakuwona, Mulungu wa Yakobe sakuzidziŵa.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Iwo amati, “Yehova sakuona; Mulungu wa Yakobo salabadirako.”

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 94:7
9 Mawu Ofanana  

Onani abwetuka pakamwa pao; m'milomo mwao muli lupanga, pakuti amati, Amva ndani?


Tsoka kwa iwo amene afunitsa kubisira Yehova uphungu wao, ndi ntchito zao zili mumdima, ndipo amati ndani ationa ife? Ndani atidziwa ife?


Pakuti wakhulupirira zoipa zako, wati, Palibe wondiona ine; nzeru zako ndi chidziwitso chako zakusandutsa woipa; ndipo wanena mumtima mwako, Ndine, ndipo popanda ine palibenso wina.


Pamenepo anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, wapenya kodi chochita akulu a nyumba ya Israele mumdima, aliyense m'chipinda chake cha zifanizo? Pakuti ati, Yehova satipenya, Yehova wataya dziko.


Pamenepo ananena nane, Mphulupulu ya nyumba ya Israele ndi Yuda ndi yaikulukulu ndithu, ndi dziko ladzala ndi mwazi, ndi mzindawo wadzala ndi kukhotetsa milandu; pakuti ati, Yehova wataya dziko, Yehova sapenya.


Ndipo kudzachitika nthawi yomweyi kuti ndidzasanthula Yerusalemu ndi nyali, ndipo ndidzalanga amunawo okhala ndi nsenga, onena m'mtima mwao, Yehova sachita chokoma, kapena kuchita choipa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa