Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 94:6 - Buku Lopatulika

6 Amapha wamasiye ndi mlendo, nawapha ana amasiye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Amapha wamasiye ndi mlendo, nawapha ana amasiye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Amapha akazi amasiye ndi alendo okhala nawo m'dziko mwao, amaphanso ana amasiye.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Amaphanso amayi a masiye ndi alendo okhala nawo mʼdziko; amapha ana amasiye.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 94:6
6 Mawu Ofanana  

kuwapatulira osowa kuchiweruziro, ndi kuchotsera anthu anga aumphawi zoyenera zao, kuti alande za akazi amasiye, nafunkhire ana amasiye!


Yehova atero: Chitani chiweruzo ndi chilungamo, landitsani ofunkhidwa m'dzanja la wosautsa; musachite choipa, musamchitire mlendo chiwawa, kapena ana amasiye, kapena akazi amasiye, musakhetse mwazi wosachimwa pamalo pano.


ndi kuleka kutsendereza mlendo, ndi wamasiye, ndi mkazi wamasiye, osakhetsa mwazi wosachimwa m'malo muno, osatsata milungu ina ndi kudziipitsa nayo;


Mwa iwe anapepula atate ndi mai, pakati pa iwe anamchitira mlendo momzunza, mwa iwe anazunza ana amasiye, ndi mkazi wamasiye.


Ndipo ndidzayandikiza kwa inu kuti ndiweruze; ndipo ndidzakhala mboni yakufulumira kutsutsa obwebweta, ndi achigololo, ndi olumbira monama; ndi iwo akunyenga wolembedwa ntchito pa kulipira kwake, akazi amasiye, ndi ana amasiye, ndi wakuipsa mlandu wa mlendo, osandiopa Ine, ati Yehova wa makamu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa