Masalimo 94:5 - Buku Lopatulika5 Aphwanya anthu anu, Yehova, nazunza cholowa chanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Aphwanya anthu anu, Yehova, nazunza cholandira chanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Amatswanya anthu anu, Inu Chauta, amazunza anthu anu osankhidwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Amaphwanya anthu anu, Inu Yehova; amapondereza cholowa chanu. Onani mutuwo |