Masalimo 94:4 - Buku Lopatulika4 Anena mau, alankhula zowawa; adzitamandira onse ochita zopanda pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Anena mau, alankhula zowawa; adzitamandira onse ochita zopanda pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Amalankhula modzikuza ndipo amanyadira zoipa zao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Amakhuthula mawu onyada; onse ochita zoyipa ndi odzaza ndi kudzikuza. Onani mutuwo |