Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 94:3 - Buku Lopatulika

3 Oipa adzatumpha ndi chimwemwe kufikira liti, Yehova? Oipa adzatero kufikira liti?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Oipa adzatumpha ndi chimwemwe kufikira liti, Yehova? Oipa adzatero kufikira liti?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Inu Chauta, kodi anthu oipa adzadzitamabe mpaka liti?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Kodi mpaka liti anthu oyipa Inu Yehova, mpaka liti anthu oyipa adzalumpha ndi chimwemwe?

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 94:3
16 Mawu Ofanana  

Nampachika Hamani pa mtengo adaukonzera Mordekai. Pamenepo mkwiyo wa mfumu unatsika.


Nati Estere, Munthu wosautsa ndi mdani ndiye Hamani woipa uyu. Pamenepo Hamani anagwidwa mantha pamaso pa mfumu ndi mkazi wamkulu.


kuti kufuula kokondwera kwa woipa sikukhalira kutha, ndi chimwemwe cha wonyoza Mulungu chikhala kamphindi?


Pakuti Inu ndinu Mulungu wa mphamvu yanga; mwanditayiranji? Ndimayenderanji woliralira chifukwa cha kundipsinja mdani?


Achita zaphwete nalankhula moipa za kusautsa, alankhula modzitama.


Yehova, mudzakwiya nthawi zonse kufikira liti? Nidzatentha nsanje yanu ngati moto?


Yehova, Mulungu wa makamu, mudzakwiyira pemphero la anthu anu kufikira liti?


Mudzabisala kosatha kufikira liti, Yehova; ndi kuzaza kwanu kudzatentha ngati moto kufikira liti?


Iwe lupanga la Yehova, atsala masiku angati osakhala chete iwe? Dzilonge wekha m'chimake; puma, nukhale chete.


Yehova, ndidzafuula mpaka liti osamva Inu? Ndifuulira kwa Inu za chiwawa, koma simupulumutsa.


ndipo anafuula ndi mau aakulu, ndi kunena, Kufikira liti, Mfumu yoyera ndi yoona, muleka kuweruza ndi kubwezera chilango chifukwa cha mwazi wathu, pa iwo akukhala padziko?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa