Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 94:11 - Buku Lopatulika

11 Yehova adziwa zolingalira za munthu, kuti zili zachabe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Yehova adziwa zolingalira za munthu, kuti zili zachabe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Chauta amadziŵa maganizo a anthu kuti ndi mpweya chabe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Yehova amadziwa maganizo a munthu; Iye amadziwa kuti maganizowo ndi achabechabe.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 94:11
9 Mawu Ofanana  

Koma, chifukwa cha Inu, tiphedwa tsiku lonse; tiyesedwa ngati nkhosa zakuzipha.


Pakuti Ine ndidziwa ntchito zao ndi maganizo ao; nthawi ikudza yakudzasonkhanitsa Ine a mitundu yonse ndi zinenedwe zonse, ndipo adzafika nadzaona ulemerero wanga.


Pakuti kulembedwa, Ndidzaononga nzeru za anzeru, ndi kuchenjera kwa ochenjera ndidzakutha.


Pakuti popeza m'nzeru ya Mulungu dziko lapansi, mwa nzeru yake, silinadziwe Mulungu, chidamkonda Mulungu kupulumutsa okhulupirirawo mwa chopusa cha kulalikira.


Chifukwa kuti chopusa cha Mulungu chiposa anthu ndi nzeru zao; ndipo chofooka cha Mulungu chiposa anthu ndi mphamvu yao.


ndiponso Ambuye azindikira zolingirira za anzeru, kuti zili zopanda pake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa