Masalimo 94:12 - Buku Lopatulika12 Wodala munthu amene mumlanga, Yehova; ndi kumphunzitsa m'chilamulo chanu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Wodala munthu amene mumlanga, Yehova; ndi kumphunzitsa m'chilamulo chanu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Inu Chauta, ngwodala munthu amene mumamlangiza, amene mumamphunzitsa ndi malamulo anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Wodala munthu amene Inu Yehova mumamulangiza, munthu amene mumamuphunzitsa kuchokera mulamulo lanu; Onani mutuwo |