Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 92:15 - Buku Lopatulika

15 kulalikira kuti Yehova ngwolunjika; Iye ndiye thanthwe langa, ndipo mwa Iye mulibe chosalungama.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 kulalikira kuti Yehova ngwolunjika; Iye ndiye thanthwe langa, ndipo mwa Iye mulibe chosalungama.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 imaonetsa kuti Chauta ndi wolungama. Iye ndiye thanthwe langa mwa Iye mulibe chokhota.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 kulengeza kuti, “Yehova ndi wolungama; Iye ndiye Thanthwe langa, ndipo mwa Iye mulibe choyipa.”

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 92:15
17 Mawu Ofanana  

Chifukwa chake mundimvere ine, eni nzeru inu, nkutali ndi Mulungu kuchita choipa, ndi Wamphamvuyonse kuchita chosalungama.


Ndiye akunga mtengo wooka pa mitsinje ya madzi; wakupatsa chipatso chake pa nyengo yake, tsamba lake lomwe losafota; ndipo zonse azichita apindula nazo.


Yehova ali wolungama m'njira zake zonse, ndi wachifundo m'ntchito zake zonse.


Yehova ndiye thanthwe langa, ndi linga langa, ndi Mpulumutsi wanga; Mulungu wanga, ngaka yanga, ndidzakhulupirira Iye; chikopa changa, nyanga ya chipulumutso changa, msanje wanga.


Iye yekhayo ndiye thanthwe langa ndi chipulumutso changa, msanje wanga, sindidzagwedezeka.


Kuopa Yehova kutanimphitsa masiku; koma zaka za oipa zidzafinimpha.


Yehova pakati pake ali wolungama; sadzachita chosalungama, m'mawa ndi m'mawa aonetsera chiweruzo chake poyera, chosasowa kanthu; koma wosalungama sadziwa manyazi.


Ndipo tsono tidzatani? Kodi chilipo chosalungama ndi Mulungu? Msatero ai.


Thanthwe, ntchito yake ndi yangwiro; pakuti njira zake zonse ndi chiweruzo; Mulungu wokhulupirika ndi wopanda chisalungamo; Iye ndiye wolungama ndi wolunjika.


Ndipo zaka zake za Mose ndizo zana limodzi ndi makumi awiri, pakumwalira iye; diso lake silinachite mdima, ndi mphamvu yake siidaleke.


m'chiyembekezo cha moyo wosatha, umene Mulungu, wosanamayo, analonjeza zisanayambe nthawi zosayamba;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa