Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 90:6 - Buku Lopatulika

6 Mamawa uphuka bwino; madzulo ausenga, nuuma.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Mamawa uphuka bwino; madzulo ausenga, nuuma.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 M'mamaŵamo umatsitsimuka ndipo umakondwa. Madzulo umafota ndi kuuma.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 ngakhale kuti mmawa umaphuka watsopano, pofika madzulo wauma ndi kufota.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 90:6
7 Mawu Ofanana  

Atuluka ngati duwa, nafota; athawa ngati mthunzi, osakhalitsa.


Koma Inu, Yehova, mukhalabe kunthawi yonse; ndi chikumbukiro chanu ku mibadwomibadwo.


Chifukwa cha liu la kubuula kwanga mnofu wanga umamatika kumafupa anga.


chakuti pophuka oipa ngati msipu, ndi popindula ochita zopanda pake; chitero kuti adzaonongeke kosatha.


Mau a wina ati, Fuula. Ndipo ndinati, Kodi ndifuule chiyani? Anthu onse ndi udzu, ndi kukoma kwao konse kunga duwa la m'thengo;


Koma ngati Mulungu aveka chotero udzu wakuthengo, ukhala lero, ndi mawa uponyedwa pamoto, nanga si inu kopambana ndithu, inu akukhulupirira pang'ono?


Pakuti latuluka dzuwa ndi kutentha kwake, ndipo laumitsa udzu; ndipo lathothoka duwa lake, ndi ukoma wa maonekedwe ake waonongeka; koteronso wachuma adzafota m'mayendedwe ake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa