Masalimo 9:7 - Buku Lopatulika7 Koma Yehova akhala chikhalire, anakonzeratu mpando wachifumu wake kuti aweruze. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Koma Yehova akhala chikhalire, anakonzeratu mpando wachifumu wake kuti aweruze. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Koma Chauta amakhala pa mpando wake waufumu nthaŵi zonse, adakhazika mpando wake kuti aziweruza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Yehova akulamulira kwamuyaya; wakhazikitsa mpando wake waufumu woweruzira. Onani mutuwo |