Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 9:8 - Buku Lopatulika

8 Ndipo Iyeyu adzaweruza dziko lapansi m'chilungamo, nadzaweruza anthu molunjika.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo Iyeyu adzaweruza dziko lapansi m'chilungamo, nadzaweruza anthu molunjika.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Iye amaweruza dziko lapansi molungama, amagamula milandu ya anthu mosakondera.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Iye adzaweruza dziko mwachilungamo; adzalamulira mitundu ya anthu mosakondera.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 9:8
15 Mawu Ofanana  

Musamatero ai, kupha olungama pamodzi ndi oipa, kuta olungama akhale monga oipa; musamatero ai; kodi sadzachita zoyenera woweruza wa dziko lonse lapansi?


Yehova ndiye Mfumu kunthawi yamuyaya; aonongeka amitundu m'dziko lake.


Yehova anakhala pa chigumula, inde Yehova akhala mfumu kunthawi yonka muyaya.


Ndipo zakumwamba zionetsera chilungamo chake; pakuti Mulungu mwini wake ndiye woweruza.


Pakuti chiweruzo chidzabwera kunka kuchilungamo, ndipo oongoka mtima onse adzachitsata.


Pamaso pa Yehova, pakuti akudza; pakuti akudza kudzaweruza dziko lapansi Adzaweruza dziko lokhalamo anthu ndi chilungamo, ndi mitundu ya anthu ndi choonadi.


Pamaso pa Yehova, popeza akudza kudzaweruza dziko lapansi; adzaweruza dziko lokhalamo anthu ndi chilungamo, ndipo mitundu ya anthu molunjika.


Ndipo mphamvu ya mfumu ikonda chiweruzo; Inu mukhazikitsa zolunjika, muchita chiweruzo ndi chilungamo mu Yakobo.


Yehova adzachita ufumu nthawi yonka muyaya.


Koma Yehova ndiye Mulungu woona; ndiye Mulungu wamoyo, mfumu yamuyaya; pa mkwiyo wake dziko lapansi lidzanthunthumira, ndi amitundu sangapirire ukali wake.


chifukwa anapangira tsiku limene adzaweruza dziko lokhalamo anthu m'chilungamo, ndi munthu amene anamuikiratu; napatsa anthu onse chitsimikizo, pamene anamuukitsa Iye kwa akufa.


tsiku limene Mulungu adzaweruza ndi Khristu Yesu zinsinsi za anthu, monga mwa Uthenga wanga Wabwino.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa