Masalimo 9:6 - Buku Lopatulika6 Adaniwo atha psiti, apululuka nthawi zonse; ndipo mizindayo mwaipasula, chikumbukiro chao pamodzi chatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Adaniwo atha psiti, apululuka nthawi zonse; ndipo midziyo mwaipasula, chikumbukiro chao pamodzi chatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Adani athu atha phu. Mwapasula mizinda yao kotheratu, anthu sadzaikumbukiranso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Chiwonongeko chosatha chagwera adani, mwafafaniza mizinda yawo; ngakhale chikumbutso chawo chawonongedwa. Onani mutuwo |