Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 88:3 - Buku Lopatulika

3 Pakuti mzimu wanga wadzala nao mavuto, ndi moyo wanga wayandikira kumanda.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Pakuti mzimu wanga wadzala nao mavuto, ndi moyo wanga wayandikira kumanda.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Pakuti mtima wanga ndi wodzaza ndi mavuto, moyo wanga ukuyandikira ku malo a anthu akufa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Pakuti ndili ndi mavuto ambiri ndipo moyo wanga ukuyandikira ku manda.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 88:3
15 Mawu Ofanana  

Inde wasendera kufupi kumanda, ndi moyo wake kwa akuononga.


Mtima wao unyansidwa nacho chakudya chilichonse; ndipo ayandikira zipata za imfa.


Akwera kuthambo, atsikira kozama; mtima wao usungunuka nacho choipacho.


Yehova, imvani chilungamo, mverani mfuu wanga; tcherani khutu ku pemphero langa losatuluka m'milomo ya chinyengo.


Tsiku la nsautso yanga ndinafuna Ambuye. Dzanja langa linatambalika usiku, losaleka; mtima wanga unakana kutonthozedwa.


Iye ananyozedwa ndi kukanidwa ndi anthu; munthu wazisoni, ndi wodziwa zowawa; ndipo ananyozedwa monga munthu wombisira anthu nkhope zao; ndipo ife sitinamlemekeze.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa