Masalimo 88:2 - Buku Lopatulika2 Pemphero langa lidze pamaso panu; munditcherere khutu kukuwa kwanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pemphero langa lidze pamaso panu; munditcherere khutu kukuwa kwanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Pemphero langa lifike kwa Inu, tcherani khutu kuti mumve kulira kwanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Pemphero langa lifike pamaso panu; tcherani khutu lanu kuti mumve kulira kwanga. Onani mutuwo |