Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 86:6 - Buku Lopatulika

6 Tcherani khutu pemphero langa, Yehova; nimumvere mau a kupemba kwanga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Tcherani khutu pemphero langa, Yehova; nimumvere mau a kupemba kwanga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Tcherani khutu, Inu Chauta, kuti mumve pemphero langa. Mverani kulira kwanga kopemba.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Yehova imvani pemphero langa; mvetserani kulira kwanga kofuna chifundo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 86:6
5 Mawu Ofanana  

Ambuye, mutcherere khutu pemphero la kapolo wanu, ndi pemphero la akapolo anu okondwera nako kuopa dzina lanu; ndipo mupambanitse kapolo wanu lero lino, ndi kumuonetsera chifundo pamaso pa munthu uyu. Koma ndinali ine wothirira mfumu chakumwa chake.


Ambuye, imvani liu langa; makutu anu akhale chimverere mau a kupemba kwanga.


Yehova, imvani chilungamo, mverani mfuu wanga; tcherani khutu ku pemphero langa losatuluka m'milomo ya chinyengo.


Tcherani khutu pemphero langa, Mulungu; ndipo musadzibisa pa kupemba kwanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa