Masalimo 85:7 - Buku Lopatulika7 Tionetseni chifundo chanu, Yehova, tipatseni chipulumutso chanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Tionetseni chifundo chanu, Yehova, tipatseni chipulumutso chanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tiwonetseni chikondi chanu chosasinthika, Inu Chauta, ndipo mutipulumutse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Tionetseni chikondi chanu chosatha, Inu Yehova, ndipo tipatseni chipulumutso chanu. Onani mutuwo |
mudzamvekanso mau akukondwa ndi mau akusekera, mau a mkwati ndi mau a mkwatibwi, mau a iwo akuti, Myamikireni Yehova wa makamu, pakuti Yehova ndiye wabwino, chifundo chake nchosatha; ndi a iwo akutengera nsembe zoyamikira m'nyumba ya Yehova. Pakuti ndidzabweza undende wa dziko monga poyamba, ati Yehova.