Masalimo 85:6 - Buku Lopatulika6 Kodi simudzatipatsanso moyo, kuti anthu anu akondwerere ndi Inu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Kodi simudzatipatsanso moyo, kuti anthu anu akondwerere ndi Inu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Kodi simudzatipatsanso moyo, kuti ife anthu anu tikondwere mwa Inu? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Kodi simudzatitsitsimutsanso, kuti anthu anu asangalale mwa Inu? Onani mutuwo |
mudzamvekanso mau akukondwa ndi mau akusekera, mau a mkwati ndi mau a mkwatibwi, mau a iwo akuti, Myamikireni Yehova wa makamu, pakuti Yehova ndiye wabwino, chifundo chake nchosatha; ndi a iwo akutengera nsembe zoyamikira m'nyumba ya Yehova. Pakuti ndidzabweza undende wa dziko monga poyamba, ati Yehova.