Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 85:13 - Buku Lopatulika

13 Chilungamo chidzamtsogolera; ndipo chidzamkonzera mapazi ake njira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Chilungamo chidzamtsogolera; nichidzamkonzera mapazi ake njira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Mulungu ndi wolungama chikhalire, chilungamo chake chimaongolera zochita zake zonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Wolungama amapita patsogolo pake ndi kukonza njira za mapazi ake.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 85:13
18 Mawu Ofanana  

Mundiyendetse mopita malamulo anu; pakuti ndikondwera m'menemo.


Chilungamo ndi chiweruzo ndiwo maziko a mpando wanu wachifumu; chifundo ndi choonadi zitsogolera pankhope panu.


Pomwepo kuunika kwako kudzawalitsa monga m'mawa, ndi kuchira kwako kudzaonekera msangamsanga; ndipo chilungamo chako chidzakutsogolera; ulemerero wa Yehova udzakhala wotchinjiriza pambuyo pako.


Ndipo ndikhutitsa moyo wa ansembe ndi mafuta, ndipo anthu anga adzakhuta ndi zokoma zanga, ati Yehova.


Ndipo ndidzachulukitsa zobala za mitengo, ndi zipatso za m'munda, kuti musalandirenso chitonzo cha njala mwa amitundu.


ndidzakupatsani mvula m'nyengo zake, ndi dziko lidzapereka zipatso zake, ndi mitengo ya m'minda idzabala zipatso zake.


Ndikupatsani inu lamulo latsopano, kuti mukondane wina ndi mnzake; monga ndakonda inu, kuti inunso mukondane wina ndi mnzake.


Koma ife tonse ndi nkhope yosaphimbika popenyerera monga mwa kalirole ulemerero wa Ambuye, tisandulika m'chithunzithunzi chomwechi kuchokera kuulemerero kunka kuulemerero, monga ngati kuchokera kwa Ambuye Mzimu.


Ndinapachikidwa ndi Khristu; koma ndili ndi moyo; wosatinso ine ai, koma Khristu ali ndi moyo mwa ine; koma moyo umene ndili nao tsopano m'thupi, ndili nao m'chikhulupiriro cha Mwana wa Mulungu, amene anandikonda, nadzipereka yekha chifukwa cha ine.


Popeza Khristu adamva zowawa m'thupi, mudzikonzere mtima womwewo; pakuti iye amene adamva zowawa m'thupi walekana nalo tchimo;


iye wakunena kuti akhala mwa Iye, ayeneranso mwini wake kuyenda monga anayenda Iyeyo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa