Masalimo 86:1 - Buku Lopatulika1 Tcherani khutu lanu Yehova, mundiyankhe; pakuti ine ndine wozunzika ndi waumphawi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Tcherani khutu lanu Yehova, mundiyankhe; pakuti ine ndine wozunzika ndi waumphawi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tcherani khutu, Inu Chauta, ndipo mundiyankhe, pakuti ndine wosauka ndi wosoŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Ndimvereni Yehova ndipo mundiyankhe, pakuti ndine wosauka ndi wosowa. Onani mutuwo |