Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 81:9 - Buku Lopatulika

9 Kwanu kusakhale mulungu wofuma kwina; nusagwadire mulungu wachilendo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Kwanu kusakhale mulungu wofuma kwina; nusagwadire mulungu wachilendo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 “Pasadzakhale mulungu wachilendo pakati panu. Musadzapembedze mulungu wina ai.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Musadzakhale ndi mulungu wachilendo pakati panu; musadzagwadire mulungu wina.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 81:9
12 Mawu Ofanana  

Ndipo anati, Chifukwa chake tamverani mau a Yehova, Ndinaona Yehova alikukhala pa mpando wake wachifumu, ndi khamu lonse lakumwamba lili chilili m'mbali mwake, ku dzanja lamanja ndi lamanzere.


Tikadaiwala dzina la Mulungu wathu, ndi kutambasulira manja athu kwa mulungu wachilendo;


Imvani, anthu anga, ndipo ndidzanena; Israele, ndipo ndidzachita mboni pa iwe, Ine Mulungu, ndine Mulungu wako.


ndipo anati, Ngati udzamveratu mau a Yehova, Mulungu wako, ndi kuchita zoona pamaso pake, ndi kutchera khutu pa malamulo ake, ndi kusunga malemba ake onse, za nthenda zonse ndinaziika pa Aejipito sindidzaziika pa iwe nnena imodzi; pakuti Ine Yehova ndine wakuchiritsa iwe.


Tcherani inu makutu, imvani mau anga; mverani, imvani kulankhula kwanga.


Ine ndalalikira, ndipo ndikupulumutsa ndi kumvetsa, ndipo panalibe Mulungu wachilendo pakati pa inu; chifukwa chake inu ndinu mboni zanga, ati Yehova, ndipo Ine ndine Mulungu.


Imvani mau a Yehova, inu ana a Israele; pakuti Yehova ali ndi mlandu ndi okhala m'dziko, popeza palibe choonadi, kapena chifundo, kapena kudziwa Mulungu m'dziko.


Yuda wachita monyenga, ndi mu Israele ndi mu Yerusalemu mwachitika chonyansa; pakuti Yuda waipsa chipatuliko cha Yehova chimene achikonda, nakwatira mwana wamkazi wa mulungu wachilendo.


Yehova yekha anamtsogolera, ndipo palibe mulungu wachilendo naye.


Musamatsate milungu ina, milungu ina ya mitundu ya anthu akuzinga inu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa