Masalimo 81:8 - Buku Lopatulika8 Tamvani, anthu anga, ndidzakuchitirani mboni; Israele, ukadzandimvera! Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Tamvani, anthu anga, ndidzakuchitirani mboni; Israele, ukadzandimvera! Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Imvani inu anthu anga, ndikulangizeni. Inu Aisraele, chonde mukadandimvera! Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 “Imvani anthu anga, ndipo ndidzakuchenjezani ngati mungathe kumvetsera, Inu Israeli! Onani mutuwo |