Masalimo 81:10 - Buku Lopatulika10 Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakukweza kukuchotsa kudziko la Ejipito; yasamitsa pakamwa pako ndipo ndidzalidzaza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakukweza kukuchotsa kudziko la Ejipito; yasamitsa pakamwa pako ndipo ndidzalidzaza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Ine ndine Chauta, Mulungu wanu, amene ndidakutulutsani m'dziko la Ejipito. Yasamani kukamwa, Ine ndidzakudyetsani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani mʼdziko la Igupto. Yasamani kukamwa kwanu ndipo ndidzakudyetsani. Onani mutuwo |