Masalimo 81:4 - Buku Lopatulika4 Pakuti ichi ndi cholemba cha kwa Israele, chiweruzo cha Mulungu wa Yakobo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pakuti ichi ndi cholemba cha kwa Israele, chiweruzo cha Mulungu wa Yakobo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Pakuti ndilo lamulo lokhalira Israele, lochokera kwa Mulungu wa Yakobe, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 ili ndi lamulo kwa Israeli, langizo la Mulungu wa Yakobo. Onani mutuwo |