Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 81:16 - Buku Lopatulika

16 Akadawadyetsa naye tirigu wokometsetsa, ndikadakukhutitsanso ndi uchi wa m'thanthwe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Akadawadyetsa naye tirigu wokometsetsa, ndikadakukhutitsanso ndi uchi wa m'thanthwe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Ndikadakudyetsani ndi ufa wosalala watirigu, ndipo ndikadakukhutitsani ndi uchi wam'thanthwe.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Koma inu mukanadyetsedwa tirigu wabwino kwambiri; ndikanakukhutitsani ndi uchi wochokera pa thanthwe.”

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 81:16
9 Mawu Ofanana  

muja popondera ine padakhatamira ndi mafuta amkaka, ndi thanthwe linanditsanulira mitsinje ya mafuta a azitona!


Ndiye amene akhalitsa malire anu mumtendere; akukhutitsani ndi tirigu wakucha bwino.


Alendo adzafota, nadzatuluka monjenjemera m'ngaka mwao.


Ndipo madwale adzakhala ndi tirigu, ndi vinyo, ndi mafuta; zidzasefuka m'zosungiramo zao.


Ha? Mwenzi akadakhala nao mtima wotere wakundiopa Ine, ndi kusunga malamulo anga masiku onse, kuti chiwakomere iwo ndi ana ao nthawi zonse!


Ndipo amuna a pamzinda anati kwa Samisoni tsiku lachisanu ndi chiwiri, lisanalowe dzuwa, Chozuna choposa uchi nchiyani; ndi champhamvu choposa mkango nchiyani? Pamenepo ananena nao, Mukadapanda kulima ndi ng'ombe yanga, simukadatha kumasulira mwambi wanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa