Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 81:13 - Buku Lopatulika

13 Ha! Akadandimvera anthu anga, akadayenda m'njira zanga Israele!

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ha! Akadandimvera anthu anga, akadayenda m'njira zanga Israele!

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 “Anthu anga akadandimvera, Aisraele akadayenda m'njira zanga,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 “Anthu anga akanangondimvera, Israeli akanatsatira njira zanga,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 81:13
8 Mawu Ofanana  

momwemo adzadya zipatso za mayendedwe ao, nadzakhuta zolingalira zao.


Mwenzi utamvera malamulo anga mtendere wako ukanakhala ngati mtsinje, ndi chilungamo chako monga mafunde a nyanja;


Koma sanamvere, sanatchere khutu, koma anayenda mu upo ndi m'kuuma kwa mtima wao woipa, nabwerera chambuyo osayenda m'tsogolo.


Ha, Yerusalemu, Yerusalemu, amene umapha aneneri, ndi kuwaponya miyala iwo otumidwa kwa iwe! Ine ndinafuna kangati kusonkhanitsa pamodzi ana ako, inde monga thadzi lisonkhanitsa anapiye ake m'mapiko ake, koma inu simunafune ai!


Akadakhala nazo nzeru, akadazindikira ichi, akadasamalira chitsirizo chao!


Ha? Mwenzi akadakhala nao mtima wotere wakundiopa Ine, ndi kusunga malamulo anga masiku onse, kuti chiwakomere iwo ndi ana ao nthawi zonse!


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa