Masalimo 81:1 - Buku Lopatulika1 Imbitsirani Mulungu ndiye mphamvu yathu; fuulirani kwa Mulungu wa Yakobo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Imbitsirani Mulungu ndiye mphamvu yathu; fuulirani kwa Mulungu wa Yakobo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Kwezani mau kuimbira Mulungu amene ali mphamvu zathu. Fuulani ndi chimwemwe kwa Mulungu wa Yakobe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Imbani mwachimwemwe kwa Mulungu mphamvu yathu; Fuwulani mokweza kwa Mulungu wa Yakobo! Onani mutuwo |