Masalimo 80:8 - Buku Lopatulika8 Mudatenga mpesa kuchokera ku Ejipito, munapirikitsa amitundu ndi kuuoka uwu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Mudatenga mpesa kuchokera ku Ejipito, munapirikitsa amitundu ndi kuuoka uwu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Mudatulutsa mpesa wanu Israele m'dziko la Ejipito. Mudapirikitsa mitundu ina ya anthu kuti muubzale mpesawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Munatulutsa mpesa kuchoka ku Igupto; munathamangitsa anthu a mitundu ina ndi kuwudzala mpesawo. Onani mutuwo |