Masalimo 80:6 - Buku Lopatulika6 Mutiika kuti atilimbirane anzathu; ndipo adani athu atiseka mwa iwo okha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Mutiika kuti atilimbirane anzathu; ndipo adani athu atiseka mwa iwo okha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Mwaŵasandutsa chinthu chonyozeka kwa anzathu a mitundu ina, ndipo adani athu akakhala pamodzi, amangotiseka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Mwachititsa kuti tikhale gwero la mikangano pakati pa anansi athu, ndipo adani athu akutinyoza. Onani mutuwo |