Masalimo 80:2 - Buku Lopatulika2 Utsani chamuna chanu pamaso pa Efuremu ndi Benjamini ndi Manase, ndipo mutidzere kutipulumutsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Utsani chamuna chanu pamaso pa Efuremu ndi Benjamini ndi Manase, ndipo mutidzere kutipulumutsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 dziwonetseni kwa mafuko a Efuremu ndi Benjamini ndi Manase. Onetsani mphamvu zanu, ndipo mubwere kudzatipulumutsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 kwa Efereimu, Benjamini ndi Manase. Utsani mphamvu yanu; bwerani ndi kutipulumutsa. Onani mutuwo |