Masalimo 80:1 - Buku Lopatulika1 Mbusa wa Israele, tcherani khutu; inu wakutsogolera Yosefe ngati nkhosa; inu wokhala pa akerubi, walitsani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Mbusa wa Israele, tcherani khutu; inu wakutsogolera Yosefe ngati nkhosa; inu wokhala pa akerubi, walitsani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Imvani, Inu Mbusa wa Israele, Inu amene mumatsogolera anthu a Yosefe ngati gulu la nkhosa. Inu amene mumakhala pa akerubi ngati pa mpando wanu wachifumu, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tcherani khutu Inu mʼbusa wa Israeli, Inu amene mumatsogolera Yosefe monga nkhosa; Inu amene mumakhala pa mpando waufumu pakati pa akerubi, walani Onani mutuwo |