Masalimo 80:13 - Buku Lopatulika13 Nguluwe zochokera kuthengo ziukumba, ndi nyama za kuchidikha ziudya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Nguluwe zochokera kuthengo ziukumba, ndi nyama za kuchidikha ziudya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Nguluŵe zam'nkhalango zimauwononga, ndipo zonse zoyenda m'thengo zimaudya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Nguluwe zochokera mʼnkhalango zikuwononga ndipo zirombo za mthengo zimawudya. Onani mutuwo |