Masalimo 80:12 - Buku Lopatulika12 Munapasuliranji maphambo ake, kotero kuti onse akupita m'njira atcherako? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Munapasuliranji maphambo ake, kotero kuti onse akupita m'njira atcherako? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Nanga chifukwa chiyani mwagumula mpanda wake, kuti opita m'njira azithyola nawo zipatso zake? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Chifukwa chiyani mwagwetsa makoma ake kuti onse amene akudutsa athyole mphesa zake? Onani mutuwo |