Masalimo 80:10 - Buku Lopatulika10 Mthunzi wake unaphimba mapiri, ndi nthambi zake zikunga mikungudza ya Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Mthunzi wake unaphimba mapiri, ndi nthambi zake zikunga mikungudza ya Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Mapiri adaphimbidwa ndi mthunzi wake, mikungudza yaikulu yomwe idaphimbidwa ndi nthambi zake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Mapiri anaphimbidwa ndi mthunzi wake, mikungudza yamphamvu ndi nthambi zake. Onani mutuwo |