Masalimo 8:5 - Buku Lopatulika5 Pakuti munamchepsa pang'ono ndi Mulungu, munamveka iye korona wa ulemerero ndi ulemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pakuti munamchepsa pang'ono ndi Mulungu, munamveka iye korona wa ulemerero ndi ulemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ndiyetu mudamlenga mochepera pang'ono kwa Mulungu amene, mudampatsa ulemerero ndi ulemu wachifumu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Inu munamupanga kukhala wocheperapo kusiyana ndi zolengedwa zakumwamba ndipo mwamuveka ulemerero ndi ulemu. Onani mutuwo |