Masalimo 79:7 - Buku Lopatulika7 Pakuti anathera Yakobo, napasula pokhalira iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Pakuti anathera Yakobo, napasula pokhalira iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Pakuti ameza anthu a Yakobe, ndipo dziko lao alisandutsa bwinja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 pakuti iwo ameza Yakobo ndi kuwononga dziko lawo. Onani mutuwo |