Masalimo 78:6 - Buku Lopatulika6 kuti mbadwo ukudzawo udziwe, ndiwo ana amene akadzabadwa; amene adzaimirira nadzafotokozera ana ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 kuti mbadwo ukudzawo udziwe, ndiwo ana amene akadzabadwa; amene adzaimirira nadzafotokozera ana ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Motero mbadwo wakutsogolo wa ana amene sanabadwebe, udzaŵadziŵa, ndipo nawonso udzafotokozera ana ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 kotero kuti mʼbado wotsatira uthe kuzidziwa, ngakhale ana amene sanabadwe, ndi kuti iwo akafotokozere ana awonso. Onani mutuwo |