Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 78:53 - Buku Lopatulika

53 Ndipo anawatsogolera mokhulupirika, kotero kuti sanaope; koma nyanja inamiza adani ao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

53 Ndipo anawatsogolera mokhulupirika, kotero kuti sanaope; koma nyanja inamiza adani ao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

53 Adaŵatsogolera bwino lomwe kotero kuti sanalikuwopa, koma nyanja idamiza adani ao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

53 Anawatsogolera bwinobwino kotero kuti analibe mantha koma nyanja inamiza adani awo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:53
9 Mawu Ofanana  

Ndipo madziwo anamiza owasautsa; sanatsale mmodzi yense.


Nakhuthula Farao ndi khamu lake mu Nyanja Yofiira: pakuti chifundo chake nchosatha.


Ndipo Mose ananena ndi anthu, Musaope, chilimikani, ndipo penyani chipulumutso cha Yehova, chimene adzakuchitirani lero; pakuti Aejipito mwawaona lerowa, simudzawaonanso konse.


Ndipo Yehova anati kwa Mose, Ufuuliranji kwa Ine? Lankhula ndi ana a Israele kuti aziyenda.


Munaombetsa mphepo yanu, nyanja inawamiza; anamira m'madzi aakulu ngati mtovu.


Ndipo Mose anamvera mau a mpongozi wake, nachita zonse adazinena.


Ndi chikhulupiriro anaoloka Nyanja Yofiira kupita ngati pamtunda: ndiko Aejipito poyesanso anamizidwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa