Masalimo 78:44 - Buku Lopatulika44 Nasanduliza nyanja yao mwazi, ndi mitsinje yao, kuti sangakhoze kumwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Nasanduliza nyanja yao mwazi, ndi mitsinje yao, kuti sangakhoze kumwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Paja Mulungu adasandutsa madzi a mitsinje yao kuti akhale magazi, kotero kuti Aejipito sadathe kumwa madziwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Iye anasandutsa mitsinje yawo kukhala magazi; Iwo sanathe kumwa madzi ochokera mʼmitsinje yawo. Onani mutuwo |