Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 78:41 - Buku Lopatulika

41 Pakuti anabwerera m'mbuyo, nayesa Mulungu, nachepsa Woyerayo wa Israele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

41 Pakuti anabwerera m'mbuyo, nayesa Mulungu, nachepsa Woyerayo wa Israele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

41 Kaŵirikaŵiri ankamuyesa, ankamputa Woyera wa Israele.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

41 Kawirikawiri iwo ankamuyesa Mulungu; ankamuputa Woyera wa Israeli.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:41
11 Mawu Ofanana  

Ndiye yani wamtonza ndi kumchitira mwano? Ndiye yani wamkwezera mau ndi kumgadamira maso ako m'mwamba? Ndiye Woyerayo wa Israele.


Pakuti chikopa chathu chifuma kwa Yehova; ndi mfumu yathu kwa Woyera wa Israele.


Mtundu wochimwa inu, anthu olemedwa ndi mphulupulu, mbeu yakuchita zoipa, ana amene achita moononga, iwo amsiya Yehova, iwo amnyoza Woyera wa Israele, iwo adana naye nabwerera m'mbuyo.


popeza anthu onse awa amene adaona ulemerero wanga, ndi zizindikiro zanga, ndidazichita mu Ejipito ndi m'chipululu, koma anandiyesa Ine kakhumi aka, osamvera mau anga;


Ndipo anati wina ndi mnzake, Tiike mtsogoleri, tibwerere ku Ejipito.


amene makolo athu sanafune kumvera iye, koma anamkankha achoke, nabwerera m'mbuyo mumtima mwao ku Ejipito,


Musamayesa Yehova Mulungu wanu, monga munamyesa mu Masa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa