Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 78:40 - Buku Lopatulika

40 Kawirikawiri nanga anapikisana ndi Iye kuchigwako, nammvetsa chisoni m'chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

40 Kawirikawiri nanga anapikisana ndi Iye kuchigwako, nammvetsa chisoni m'chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

40 Kaŵirikaŵiri ankamuukira m'chipululu, ankamumvetsa chisoni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

40 Nthawi zambiri iwo ankamuwukira Iye mʼchipululu ndi kumumvetsa chisoni mʼdziko lopanda kanthu!

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:40
12 Mawu Ofanana  

popeza anapikisana nao mau a Mulungu, napeputsa uphungu wa Wam'mwambamwamba;


Koma anaonjeza kumchimwira Iye, kupikisana ndi Wam'mwambamwamba m'chipululu.


Ndi kuti asange makolo ao, ndiwo mbadwo woukirana ndi wopikisana ndi Mulungu; mbadwo wosakonza mtima wao, ndi mzimu wao sunakhazikike ndi Mulungu.


Koma iwo anapandukira ndi kumvetsa chisoni mzimu wake woyera, chifukwa chake Iye anasandulika mdani wao, nawathira nkhondo Iye yekha.


Ndipo iye anati, Mverani inu tsopano, inu a nyumba ya Davide; kodi ndi kanthu kakang'ono kwa inu kutopetsa anthu, kuti inu mutopetsa Mulungu wanga?


Ndipo Yehova anati kwa Mose, Anthu awa adzaleka liti kundinyoza? Ndipo adzayamba liti kundikhulupirira, chinkana zizindikiro zonse ndinazichita pakati pao?


Ndipo musamvetse chisoni Mzimu Woyera wa Mulungu, amene munasindikizidwa chizindikiro mwa Iye, kufikira tsiku la maomboledwe.


Kumbukirani, musamaiwala, kuti munakwiyitsa Yehova Mulungu wanu m'chipululu; kuyambira tsikuli munatuluka m'dziko la Ejipito, kufikira munalowa m'malo muno munapikisana ndi Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa