Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 78:42 - Buku Lopatulika

42 Sanakumbukire dzanja lake, tsikuli anawaombola kwa msautsi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

42 Sanakumbukire dzanja lake, tsikuli anawaombola kwa msautsi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

42 Sadakumbukire mphamvu zake kapena tsiku limene adaŵaombola kwa adani ao,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

42 Sanakumbukire mphamvu zake, tsiku limene Iye anawawombola kwa ozunza,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:42
11 Mawu Ofanana  

Anaiwala Mulungu Mpulumutsi wao, amene anachita zazikulu mu Ejipito;


Ndipo anaiwala zochita Iye, ndi zodabwitsa zake zimene anawaonetsa.


Ndipo chizikhala ndi iwe ngati chizindikiro padzanja lako, ndi chikumbutso pakati pamaso ako; kuti chilamulo cha Yehova chikhale m'kamwa mwako; pakuti Yehova anakutulutsa mu Ejipito ndi dzanja lamphamvu.


Si awa mauwo tinalankhula nanu mu Ejipito ndi kuti, Tilekeni, kuti tigwirire ntchito Aejipito? Pakuti kutumikira Aejipito kutikomera si kufa m'chipululu ai.


Ndipo padzakhala tsiku lomwelo, kuti Ambuye adzabweza kachiwiri ndi dzanja lake anthu ake otsala ochokera ku Asiriya, ndi ku Ejipito, ndi ku Patirosi, ndi ku Kusi, ndi ku Elamu, ndi ku Sinara, ndi ku Hamati, ndi ku zisumbu za m'nyanja.


ndipo munatulutsa anthu anu Israele m'dziko la Ejipito ndi zizindikiro, ndi zodabwitsa, ndi dzanja lamphamvu, ndi mkono wotambasuka, ndi mantha ambiri;


Ndi ana a Israele sanakumbukire Yehova Mulungu wao, amene anawapulumutsa m'dzanja la adani ao onse pozungulira ponse;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa