Masalimo 78:10 - Buku Lopatulika10 Sanasunga chipangano cha Mulungu, nakana kuyenda m'chilamulo chake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Sanasunga chipangano cha Mulungu, nakana kuyenda m'chilamulo chake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 sadasunge chipangano cha Mulungu, koma adakana kutsata malamulo ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 iwo sanasunge pangano la Mulungu ndipo anakana kukhala mʼmoyo wotsatira lamulo lake. Onani mutuwo |