Masalimo 78:9 - Buku Lopatulika9 Ana a Efuremu okhala nazo zida, oponya nao mauta, anabwerera m'mbuyo tsiku la nkhondo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ana a Efuremu okhala nazo zida, oponya nao mauta, anabwerera m'mbuyo tsiku la nkhondo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ngakhale Aefuremu anali ndi mauta, komabe adathaŵa pa tsiku la nkhondo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Anthu a ku Efereimu, ngakhale ananyamula mauta, anathawabe pa nthawi ya nkhondo; Onani mutuwo |